Ekisodo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+ Deuteronomo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muzigwiritsa ntchito miyala yathunthu pomangira Yehova Mulungu wanu guwa lansembe, ndipo muzipereka nsembe zopsereza kwa Yehova Mulungu wanu paguwalo.+
25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+
6 Muzigwiritsa ntchito miyala yathunthu pomangira Yehova Mulungu wanu guwa lansembe, ndipo muzipereka nsembe zopsereza kwa Yehova Mulungu wanu paguwalo.+