1 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+