Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka. Salimo 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha chisoni, moyo wanga watha,+Ndipo chifukwa cha kuusa moyo kwanga, zaka zanga zafika kumapeto.+Chifukwa cha zolakwa zanga, mphamvu zanga zafooka,+Ndipo mafupa anga afooka.+ Salimo 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndinati: “Inu Yehova, ndikomereni mtima.+Ndichiritseni, pakuti ndakuchimwirani.”+ Salimo 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititseni kumva kufuula kokondwera ndi kosangalala,+Kuti munthu* amene mwamuthyola akondwere.+
2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka.
10 Chifukwa cha chisoni, moyo wanga watha,+Ndipo chifukwa cha kuusa moyo kwanga, zaka zanga zafika kumapeto.+Chifukwa cha zolakwa zanga, mphamvu zanga zafooka,+Ndipo mafupa anga afooka.+