Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka. Salimo 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Palibe pabwino m’thupi langa chifukwa cha chidzudzulo chanu.+Ndipo m’mafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+ Salimo 147:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye amachiritsa+ anthu osweka mtima,+Ndipo amamanga zilonda zawo zopweteka.+ Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
2 Ndikomereni mtima, inu Yehova, chifukwa ndikulefuka.+Ndichiritseni,+ inu Yehova, chifukwa mafupa anga agwedezeka.
3 Palibe pabwino m’thupi langa chifukwa cha chidzudzulo chanu.+Ndipo m’mafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+