Salimo 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinakhala chete.+ Sindinatsegule pakamwa panga,+Pakuti inu munachitapo kanthu.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+ Maliro 3:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zinthu zoipa ndi zabwino sizitulukira limodzi pakamwa pa Wam’mwambamwamba.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+