Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete. Yobu 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ine tsopano ndakhala wopanda pake.+Kodi ndingakuyankheni chiyani?Ndaika dzanja langa pakamwa.+
3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.