2 Samueli 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+ Danieli 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+
10 Koma mfumu inati: “Ndili nanu chiyani+ inu ana a Zeruya?+ Musiyeni anyoze+ chifukwa Yehova wamuuza kuti,+ ‘Munyoze Davide!’ Choncho ndani angamufunse kuti, ‘N’chifukwa chiyani iwe wachita zimenezi?’”+
35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+