Salimo 67:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lapansi,+Kuti chipulumutso chanu chidziwike pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Machitidwe 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.
2 Kuti njira zanu zidziwike padziko lapansi,+Kuti chipulumutso chanu chidziwike pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.