Machitidwe 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Inu anthu a ku Yudeya ndi inu nonse a mu Yerusalemu, dziwani izi ndipo mvetserani mosamala zimene ndikufuna kukuuzani.
14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Inu anthu a ku Yudeya ndi inu nonse a mu Yerusalemu, dziwani izi ndipo mvetserani mosamala zimene ndikufuna kukuuzani.