Machitidwe 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.
14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.