Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 66:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Inu anthu nonse padziko lapansi, fuulirani Mulungu mosangalala chifukwa wapambana.+

  • Salimo 98:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova wachititsa chipulumutso chake kudziwika.+

      Chilungamo chake wachisonyeza ku mitundu ya anthu.+

  • Yesaya 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno iye anati: “Si nkhani yochepa kuti iweyo wakhala mtumiki wanga, n’cholinga choti ubwezeretse mafuko a Yakobo ndi kubweza Aisiraeli amene ali otetezeka.+ Ndakupereka kuti ukhale kuwala kwa mitundu ya anthu,+ kuti chipulumutso changa chifike mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Luka 2:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chifukwa maso anga aona njira yanu yopulumutsira+

  • Machitidwe 28:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+

  • Tito 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Mulungu waonetsa+ kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene kumabweretsa chipulumutso+ kwa anthu, kaya akhale a mtundu wotani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena