Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+
4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+