-
Salimo 46:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 N’chifukwa chake sitidzaopa, ngakhale dziko lapansi litasintha,+
Ndiponso ngakhale mapiri atagwedezeka ndi kumira m’nyanja yaikulu.+
-