Oweruza 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Yehova anayamba kusokoneza+ ndi kuwononga Sisera ndi magaleta ake onse ankhondo, pamodzi ndi anthu ake onse. Anawasokoneza ndi kuwawononga ndi lupanga pamaso pa Baraki. Zitatero Sisera anatsika m’galeta wake n’kuyamba kuthawa wapansi.
15 Pamenepo Yehova anayamba kusokoneza+ ndi kuwononga Sisera ndi magaleta ake onse ankhondo, pamodzi ndi anthu ake onse. Anawasokoneza ndi kuwawononga ndi lupanga pamaso pa Baraki. Zitatero Sisera anatsika m’galeta wake n’kuyamba kuthawa wapansi.