Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Malaki 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Koma inu amene mukuopa dzina langa, dzuwa la chilungamo lidzakuwalirani+ ndipo m’mapiko mwake mudzakhala mphamvu yochiritsa.+ Inu mudzanyamuka ndi kudumphadumpha ngati ana a ng’ombe amphongo onenepa.”+

  • Mateyu 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo, ndipo nkhope yake inawala ngati dzuwa.+ Malaya ake akunja anawala kwambiri.+

  • Chivumbulutso 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 M’dzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena