Salimo 110:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+ Danieli 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya. Mateyu 13:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+
3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+
3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.
43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+