Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+

  • Salimo 91:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+

      Inenso ndidzamupulumutsa.+

      Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+

  • Salimo 97:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+

      Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+

      Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+

  • Aroma 8:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+

  • 1 Akorinto 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma ngati munthu akukonda Mulungu,+ ameneyo amadziwika kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena