Machitidwe 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anachita zimenezi kuti anthuwo afunefune Mulungu,+ amufufuzefufuze ndi kumupezadi,+ ngakhale kuti kwenikweni, iye sali kutali ndi aliyense wa ife. Aroma 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amaposadi ena kwambiri m’njira iliyonse. Choyamba, chifukwa chakuti mawu opatulika a Mulungu+ anaikidwa m’manja mwa Ayuda.
27 Anachita zimenezi kuti anthuwo afunefune Mulungu,+ amufufuzefufuze ndi kumupezadi,+ ngakhale kuti kwenikweni, iye sali kutali ndi aliyense wa ife.
2 Iye amaposadi ena kwambiri m’njira iliyonse. Choyamba, chifukwa chakuti mawu opatulika a Mulungu+ anaikidwa m’manja mwa Ayuda.