Salimo 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu wakhala mfumu ya mitundu ya anthu.+Mulungu wakhala pampando wake wachifumu wopatulika.+ Chivumbulutso 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo wokhala pampando wachifumu+ anati: “Taonani! Zinthu zonse zimene ndikupanga n’zatsopano.”+ Ananenanso kuti: “Lemba, pakuti mawu awa ndi odalirika ndi oona.”
5 Ndipo wokhala pampando wachifumu+ anati: “Taonani! Zinthu zonse zimene ndikupanga n’zatsopano.”+ Ananenanso kuti: “Lemba, pakuti mawu awa ndi odalirika ndi oona.”