1 Akorinto 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ntchito zonsezi, mzimu umodzimodziwo+ ndiwo umazichita, pogawira+ aliyense payekha malinga ndi chifuniro cha mzimuwo.+ Aefeso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+ Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
11 Koma ntchito zonsezi, mzimu umodzimodziwo+ ndiwo umazichita, pogawira+ aliyense payekha malinga ndi chifuniro cha mzimuwo.+
9 moti anatiululira chinsinsi chopatulika+ cha chifuniro chake. Chinsinsicho n’chogwirizana ndi zokomera mwiniwakeyo ndiponso zimene anafuna mumtima mwake,+
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+