Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti mwa kukoma mtima kwakukulu kumene ndinapatsidwa, ndikuuza aliyense wa inu kumeneko kuti musamadziganizire kuposa mmene muyenera kudziganizira.+ Koma aliyense aziganiza m’njira yakuti akhale munthu woganiza bwino,+ malinga ndi chikhulupiriro+ chimene Mulungu wamupatsa.+

  • 1 Akorinto 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo.+ Komabe, aliyense ali ndi mphatso+ yake yochokera kwa Mulungu. Wina m’njira iyi, winanso m’njira inayo.

  • Aefeso 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano aliyense wa ife anapatsidwa kukoma mtima kwakukulu+ malinga ndi mmene Khristu anamuyezera mphatso yaulereyi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena