Aroma 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero, popeza kuti tili ndi mphatso zosiyanasiyana+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene tinapatsidwa, kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tilosere malinga ndi chikhulupiriro chimene tapatsidwa. 1 Akorinto 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ntchito zonsezi, mzimu umodzimodziwo+ ndiwo umazichita, pogawira+ aliyense payekha malinga ndi chifuniro cha mzimuwo.+ 2 Akorinto 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tikuyamika Mulungu chifukwa cha mphatso yake yaulere, imene sitingathe n’komwe kuifotokoza.+
6 Chotero, popeza kuti tili ndi mphatso zosiyanasiyana+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu+ kumene tinapatsidwa, kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tilosere malinga ndi chikhulupiriro chimene tapatsidwa.
11 Koma ntchito zonsezi, mzimu umodzimodziwo+ ndiwo umazichita, pogawira+ aliyense payekha malinga ndi chifuniro cha mzimuwo.+