Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kapena kodi Mulungu anayamba wapitapo kukadzitengera mtundu wa anthu pakati pa mtundu wina ndi mayesero,+ zizindikiro,+ zozizwitsa,+ nkhondo,+ dzanja lamphamvu,+ mkono wotambasula,+ ndi zoopsa zazikulu+ zofanana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona?

  • Salimo 71:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+

      Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+

      Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+

  • Danieli 6:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iye amapulumutsa ndi kulanditsa anthu ake,+ ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba+ ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”

  • Aroma 11:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena