Deuteronomo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ ndi mkono wotambasula,+ zoopsa zazikulu,+ zizindikiro ndi zozizwitsa.+ Salimo 78:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+ Yeremiya 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+
8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ ndi mkono wotambasula,+ zoopsa zazikulu,+ zizindikiro ndi zozizwitsa.+
49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+
21 Inu munatulutsa anthu anu Aisiraeli m’dziko la Iguputo+ pogwiritsa ntchito zizindikiro, zozizwitsa,+ dzanja lamphamvu, mkono wotambasula ndi zinthu zochititsa mantha kwambiri.+