Deuteronomo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula,+ zinthu zochititsa mantha, zizindikiro ndiponso zodabwitsa.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:8 Nsanja ya Olonda,10/15/2015, ptsa. 4-5
8 Pamapeto pake Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu ndi mkono wotambasula,+ zinthu zochititsa mantha, zizindikiro ndiponso zodabwitsa.+