Deuteronomo 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+ Salimo 77:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzakumbukira zochita za Ya,+Ndithu ndidzakumbukira ntchito yanu yodabwitsa yakale.+
18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+