Salimo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzalengeza dzina lanu+ kwa abale anga.+Ndidzakutamandani pakati pa mpingo.+ Salimo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+ Salimo 111:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Ndidzatamanda Yehova ndi mtima wanga wonse,+ב [Behth]Pakati pa gulu+ la owongoka mtima ndi pamsonkhano wawo.+ Aheberi 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamene akunena kuti: “Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga. Ndidzakutamandani mwa kuimba nyimbo pakati pa mpingo.”+
9 Ndanena za uthenga wabwino wachilungamo mumpingo waukulu.+Onani! Sindinatseke pakamwa panga.+Inu Yehova, mukudziwa bwino zimenezi.+
111 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Ndidzatamanda Yehova ndi mtima wanga wonse,+ב [Behth]Pakati pa gulu+ la owongoka mtima ndi pamsonkhano wawo.+
12 pamene akunena kuti: “Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga. Ndidzakutamandani mwa kuimba nyimbo pakati pa mpingo.”+