2 Mbiri 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kore mwana wa Imuna Mlevi anali mlonda wa pachipata+ chakum’mawa+ amene anali kuyang’anira zopereka zaufulu+ zopita kwa Mulungu woona ndi kugawa zopereka za Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+
14 Kore mwana wa Imuna Mlevi anali mlonda wa pachipata+ chakum’mawa+ amene anali kuyang’anira zopereka zaufulu+ zopita kwa Mulungu woona ndi kugawa zopereka za Yehova+ ndi zinthu zopatulika koposa.+