Numeri 29:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘Muzipereka zimenezi kwa Yehova pa zikondwerero zanu.+ Muzizipereka kuwonjezera pa zopereka zanu zalonjezo,+ ndi nsembe zanu zaufulu+ zimene mumapereka monga nsembe zanu zopsereza,+ nsembe zanu zambewu,+ nsembe zanu zachakumwa,+ ndi nsembe zanu zachiyanjano.’”+ Deuteronomo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo. Deuteronomo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+
39 “‘Muzipereka zimenezi kwa Yehova pa zikondwerero zanu.+ Muzizipereka kuwonjezera pa zopereka zanu zalonjezo,+ ndi nsembe zanu zaufulu+ zimene mumapereka monga nsembe zanu zopsereza,+ nsembe zanu zambewu,+ nsembe zanu zachakumwa,+ ndi nsembe zanu zachiyanjano.’”+
6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo.
10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+