Numeri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Azikakhala wokwanira gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Vinyoyo muzikam’pereka limodzi ndi nsembe yopsereza, kapena ndi nsembe ya mwana wa nkhosa wamphongo.
5 Ndipo muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Azikakhala wokwanira gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Vinyoyo muzikam’pereka limodzi ndi nsembe yopsereza, kapena ndi nsembe ya mwana wa nkhosa wamphongo.