Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Muziipereka pamodzi ndi nsembe yachakumwa+ chokwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini. Pa mwana wa nkhosa wamphongo+ aliyense muzipereka nsembe yachakumwa. Muzithirira Yehova nsembe yachakumwa choledzeretsayo+ m’malo oyera.

  • Numeri 28:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Panyama iliyonse yoperekedwa nsembe muziperekanso nsembe yachakumwa. Ng’ombe yamphongo muziipereka limodzi ndi vinyo wokwana hafu+ ya muyezo wa hini. Nkhosa yamphongo muziipereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu+ a muyezo wa hini. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo muzim’pereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo anayi+ a muyezo wa hini. Zinthu zimenezi muzizipereka monga nsembe yopsereza ya mwezi ndi mwezi, yoperekedwa mwezi uliwonse pa miyezi yonse ya pa chaka.+

  • 2 Timoteyo 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ine ndayamba kale kukhuthulidwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndipo nthawi yakuti ndimasuke+ yatsala pang’ono kukwana.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena