Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiponso muzikapereka vinyo monga nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwanira hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.

  • Numeri 28:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Panyama iliyonse yoperekedwa nsembe muziperekanso nsembe yachakumwa. Ng’ombe yamphongo muziipereka limodzi ndi vinyo wokwana hafu+ ya muyezo wa hini. Nkhosa yamphongo muziipereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu+ a muyezo wa hini. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo muzim’pereka limodzi ndi vinyo wokwana gawo limodzi mwa magawo anayi+ a muyezo wa hini. Zinthu zimenezi muzizipereka monga nsembe yopsereza ya mwezi ndi mwezi, yoperekedwa mwezi uliwonse pa miyezi yonse ya pa chaka.+

  • Deuteronomo 14:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndalamazo udzagulire chilichonse chimene mtima wako wakhumba,+ kaya ndi ng’ombe, nkhosa, mbuzi, vinyo, chakumwa choledzeretsa+ ndi chilichonse chimene mtima wako wafuna. Ndipo uzidzadya zinthuzi pamaso pa Yehova Mulungu wako ndi kukondwera,+ iweyo ndi banja lako.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena