Levitiko 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova. 1 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+ Ezara 2:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Atsogoleri ena+ a nyumba za makolo awo+ atafika kunyumba ya Yehova+ imene inali ku Yerusalemu,+ anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwe pamalo ake.+
38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.
9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+
68 Atsogoleri ena+ a nyumba za makolo awo+ atafika kunyumba ya Yehova+ imene inali ku Yerusalemu,+ anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwe pamalo ake.+