Ekisodo 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Nonse mupereke zopereka kwa Yehova.+ Aliyense amene ali ndi mtima wofunitsitsa+ apereke kwa Yehova zinthu monga golide, siliva, mkuwa,+ 1 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 golide wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, ndi siliva woti amisiri adzagwirire ntchito zonse. Ndani lero ali wokonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+ Nehemiya 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+ 2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+
5 ‘Nonse mupereke zopereka kwa Yehova.+ Aliyense amene ali ndi mtima wofunitsitsa+ apereke kwa Yehova zinthu monga golide, siliva, mkuwa,+
5 golide wopangira zinthu zagolide, siliva wopangira zinthu zasiliva, ndi siliva woti amisiri adzagwirire ntchito zonse. Ndani lero ali wokonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+
70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+