Numeri 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo atsogoleri a Isiraeli,+ amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anapereka zopereka zawo.+ Anatero monga atsogoleri a mafuko awo, monganso oyang’anira anthu amene anawerengedwa aja. Ezara 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno atsogoleri+ a mabanja a fuko la Yuda, la Benjamini, ansembe, ndi Alevi, aliyense amene Mulungu woona analimbikitsa mtima wake,+ ananyamuka kuti apite kukamanganso nyumba ya Yehova,+ yomwe inali ku Yerusalemu.
2 Pamenepo atsogoleri a Isiraeli,+ amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anapereka zopereka zawo.+ Anatero monga atsogoleri a mafuko awo, monganso oyang’anira anthu amene anawerengedwa aja.
5 Ndiyeno atsogoleri+ a mabanja a fuko la Yuda, la Benjamini, ansembe, ndi Alevi, aliyense amene Mulungu woona analimbikitsa mtima wake,+ ananyamuka kuti apite kukamanganso nyumba ya Yehova,+ yomwe inali ku Yerusalemu.