Ekisodo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Anthu inu mulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene mtima wake wamulimbikitsa.+ Ekisodo 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atsogoleri anabweretsa miyala ya onekisi ndi miyala yozika pa efodi ndi pachovala pachifuwa,+ Nehemiya 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Anthu inu mulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene mtima wake wamulimbikitsa.+
70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+