Ekisodo 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Nonse mupereke zopereka kwa Yehova.+ Aliyense amene ali ndi mtima wofunitsitsa+ apereke kwa Yehova zinthu monga golide, siliva, mkuwa,+ 1 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+ 2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+
5 ‘Nonse mupereke zopereka kwa Yehova.+ Aliyense amene ali ndi mtima wofunitsitsa+ apereke kwa Yehova zinthu monga golide, siliva, mkuwa,+
9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, pakuti anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wathunthu.+ Nayonso mfumu Davide inasangalala kwambiri.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+