Ekisodo 35:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwamuna ndi mkazi aliyense wofunitsitsa kupereka kenakake ku ntchito zonse zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose, anachita zimenezo. Ana a Isiraeli anabweretsa nsembe yaufulu kwa Yehova.+
29 Mwamuna ndi mkazi aliyense wofunitsitsa kupereka kenakake ku ntchito zonse zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose, anachita zimenezo. Ana a Isiraeli anabweretsa nsembe yaufulu kwa Yehova.+