Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 36:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo anauza Mose kuti: “Anthu akubweretsa zinthu zambiri kuposa zimene zikufunikira pa ntchito imene Yehova walamula kuti ichitike.”

  • Ezara 2:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 Atsogoleri ena+ a nyumba za makolo awo+ atafika kunyumba ya Yehova+ imene inali ku Yerusalemu,+ anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwe pamalo ake.+

  • 2 Akorinto 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika+ kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena