Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Upange chovala pachifuwa chachiweruzo+ chopeta mwaluso. Uchipange mwaluso mofanana ndi efodi. Uchipange ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+

  • Ekisodo 28:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Ndipo Aroni azinyamula mayina a ana a Isiraeli pamtima pake, pachovala pachifuwa chachiweruzo, pamene akulowa m’Malo Oyera kuti chikhale chikumbutso pamaso pa Yehova nthawi zonse.

  • Ekisodo 28:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndiyeno uike Urimu+ ndi Tumimu m’chovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamalowa kukaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula ziweruzo+ za ana a Isiraeli pamtima pake poonekera kwa Yehova nthawi zonse.

  • Ekisodo 39:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo pachovala pachifuwa anapangapo matcheni agolide woyenga bwino, okhala ngati zingwe zopota mwaluso.+

  • Ekisodo 39:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Atatero anamanga chovala pachifuwacho ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chinalowa m’mphete za chovala pachifuwa ndi mphete za efodi, kuti chovala pachifuwacho chizikhala pamwamba pa lamba wa efodi, kutinso chisasunthe pa efodipo, monga mmene Yehova analamulira Mose.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena