-
Yesaya 58:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma tsiku ndi tsiku iwo anali kufunafuna ineyo. Anali kunena kuti amasangalala kudziwa njira zanga,+ ngati mtundu umene unali kuchita zolungama ndiponso ngati mtundu umene sunasiye chilungamo cha Mulungu wawo.+ Iwo ankangokhalira kundipempha chiweruzo cholungama, ndipo anali kuyandikira kwa Mulungu amene anali kumukonda.+
-