Levitiko 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+ Aheberi 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe.+ Ndiye chifukwa chake kunali kofunika kuti uyunso akhale ndi chinachake chopereka.+
6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+
3 Pakuti mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe.+ Ndiye chifukwa chake kunali kofunika kuti uyunso akhale ndi chinachake chopereka.+