Levitiko 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Lamulo la nsembe ya kupalamula+ lili motere: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+ Levitiko 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako wansembeyo azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo imodzi ndi kuipereka monga nsembe ya kupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi+ wa mafuta uja. Zimenezi aziziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova. Levitiko 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamunayo azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe ya kupalamula+ pakhomo la chihema chokumanako. Numeri 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthuyo ayambirenso masiku ake odzipereka kwa Yehova ngati Mnaziri,+ ndipo abweretse nkhosa yaing’ono yamphongo yosapitirira chaka chimodzi monga nsembe ya kupalamula.+ Masiku oyamba aja sadzawerengedwa chifukwa anaipitsa unaziri wake.
12 Kenako wansembeyo azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo imodzi ndi kuipereka monga nsembe ya kupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi+ wa mafuta uja. Zimenezi aziziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.
21 Mwamunayo azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe ya kupalamula+ pakhomo la chihema chokumanako.
12 Munthuyo ayambirenso masiku ake odzipereka kwa Yehova ngati Mnaziri,+ ndipo abweretse nkhosa yaing’ono yamphongo yosapitirira chaka chimodzi monga nsembe ya kupalamula.+ Masiku oyamba aja sadzawerengedwa chifukwa anaipitsa unaziri wake.