Levitiko 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kenako wansembe azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo ya nsembe ya kupalamula,+ ndi muyezo umodzi wa mafuta uja, ndipo wansembeyo aziweyulira zinthu zimenezi uku ndi uku, monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+
24 “Kenako wansembe azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo ya nsembe ya kupalamula,+ ndi muyezo umodzi wa mafuta uja, ndipo wansembeyo aziweyulira zinthu zimenezi uku ndi uku, monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+