Levitiko 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako wansembeyo azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo imodzi ndi kuipereka monga nsembe ya kupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi+ wa mafuta uja. Zimenezi aziziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.
12 Kenako wansembeyo azitenga nkhosa yaing’ono yamphongo imodzi ndi kuipereka monga nsembe ya kupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi+ wa mafuta uja. Zimenezi aziziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula+ yoperekedwa kwa Yehova.