Levitiko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula. Levitiko 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye angadye mkate wa Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+
17 Pophika, musaikemo chofufumitsa chilichonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zotentha ndi moto.+ Zimenezi n’zopatulika+ koposa mofanana ndi nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.
22 Iye angadye mkate wa Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+