Ekisodo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndipo azimanga chovala pachifuwa ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chilowe mumphete za chovala pachifuwa ndi mphete za efodi, kuti chovala pachifuwacho chizikhala pamwamba pa lamba wa efodi, kutinso chisasunthe pa efodipo.+
28 Ndipo azimanga chovala pachifuwa ndi chingwe chabuluu. Chingwe chimenecho chilowe mumphete za chovala pachifuwa ndi mphete za efodi, kuti chovala pachifuwacho chizikhala pamwamba pa lamba wa efodi, kutinso chisasunthe pa efodipo.+