2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo utenge ndodo+ ya fuko lililonse kwa mtsogoleri+ wa fukolo. Zikhalepo ndodo 12. Pandodo iliyonse ulembepo dzina la mtsogoleri wa fukolo.
11 Yahati anali mtsogoleri wawo, ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anakhala nyumba imodzi ya makolo+ ndiponso gulu limodzi lokhala ndi udindo wofanana.