-
1 Mbiri 24:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma ana a Eleazara anapezeka kuti anali ndi atsogoleri ambiri kuposa ana a Itamara. Choncho ana a Eleazara, omwe anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anawagawa m’magulu 16. Ndiponso ana a Itamara, omwe anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, anawagawa m’magulu 8.
-