Ekisodo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Ulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene akufunitsitsa kupereka.+
2 “Uza Aisiraeli kuti apereke zopereka kwa ine. Ulandire zopereka zanga kwa munthu aliyense amene akufunitsitsa kupereka.+